Comfort Hardware & One Stop Shop/Solution

Comfort Hardware & One Stop Shop/Solution We are a hardware store selling items like cement, iron sheets, lime and reinforcement steels. We are located in chipoka (ginnery) opposite Blantyre stage.

25/12/2025
๐Ÿ”ฅ TAONANI! TAONANI! ๐Ÿ”ฅNkhani yabwino ya nyengo ya Christmas ๐ŸŽ„ yafika!Comfort Hardware โ€“ Chipoka yagwetsa mtengo wa Akshar...
19/12/2025

๐Ÿ”ฅ TAONANI! TAONANI! ๐Ÿ”ฅ
Nkhani yabwino ya nyengo ya Christmas ๐ŸŽ„ yafika!

Comfort Hardware โ€“ Chipoka yagwetsa mtengo wa Akshar Portland Cement ๐Ÿšง
โžก๏ธ K35,800 yokha basi!

Musaphonye mwayi uwu!
Pezani cement yoyenera kumanga yolimba komanso yodalirika pamtengo wotsika kwambiri.

๐Ÿ“ Tili ku Chipoka, moyangโ€™anana ndi Blantyre Stage
๐Ÿ“… Kuyambira lero 19 December โ€“ nyengo ya ma deals a Christmas!

๐Ÿ“ž Imbani kapena WhatsApp: 0995 917 133
Bwerani bwerani !

Comfort Hardware โ€“ Kumanga molimba, pamtengo wotsika. ๐Ÿ’ช๐Ÿ—๏ธ

Masana abwino okondedwa makasitomala athu!Ku Comfort Hardware, tili okondwa kukudziwitsani kuti takuza mndandanda wathu ...
09/12/2025

Masana abwino okondedwa makasitomala athu!

Ku Comfort Hardware, tili okondwa kukudziwitsani kuti takuza mndandanda wathu wa simenti kuti tikupatseni mitundu yosiyanasiyana ya simenti yabwino kwambiri pa mitengoso yabwino.

Tsopano tili ndi Duracrete 32.5N Cement, yopangidwa ndi Portland Cement Ltd (Lafarge), yomwe tikupezeka nayo pa mtengo wa K34,500 pa thumba!
Simenti yapamwamba kwambiri pa mtengo wotsika kwambiri.

Osadandaula, Akshar Portland Cement yomwe mumakhulupirira iliponso bwinobwino, ndipo ikugulitsidwa pa mtengo wa K37,500 pa thumba.
Chisankho chanu,ntchito yanu - udindo wathu.

Tipezeni pa Chipoka Ginnery Trading, moyang'anana ndi Blantyre Stage, kapena tiyimbireni pa 0995 917 133 (Call/WhatsApp) kuti muyitanitse kapena kufunsa katundu.

Comfort Hardware โ€“ Timange Limodzi.

Good afternoon, our valued customers!At Comfort Hardware, we are excited to announce that we have expanded our cement ra...
09/12/2025

Good afternoon, our valued customers!
At Comfort Hardware, we are excited to announce that we have expanded our cement range to give you even more quality choices at unbeatable prices.

We now have Duracrete 32.5N Cementโ€”proudly manufactured by Portland Cement Ltd (Lafarge)โ€”available at only K34,500 per bag!
A high-quality product at an incredibly affordable price.

And donโ€™t worryโ€”your trusted Akshar Portland Cement is still in stock, going at K37,500 per bag.
Your choice, your projectโ€”our duty.

Visit us at Chipoka Ginnery Trading, opposite Blantyre Stage, or contact us on 0995 917 133 (Call/WhatsApp) for orders and inquiries.

Comfort Hardware โ€“ Building Together.

01/12/2025
Choose Excellence. Choose Trust. Choose Us!โ€At Comfort, we donโ€™t just deliver quality โ€” we deliver integrity. As a fully...
01/12/2025

Choose Excellence. Choose Trust. Choose Us!โ€
At Comfort, we donโ€™t just deliver quality โ€” we deliver integrity. As a fully tax-compliant business, we proudly pay our taxes, contributing to the growth and development of our nation.

When you buy from us, youโ€™re not just getting exceptional products/services โ€” youโ€™re supporting a business that values responsibility, transparency, and community.

Buy with confidence. Buy for a better tomorrow. Buy from us!

29/11/2025

Muvutikiranji kulipira zambiri pamene mungamange ndi mtengo wotsika โ€” pafupi nanu ?
Comfort Hardware yakubweretserani mitengo yabwino ya zinthu zapamwamba pano pa Chipoka, Ginnery Trading (moyang'anana ndi Blantyre Stage).

๐Ÿ—๏ธ Cement ya Akshar Portland โ€” K37,500 pa thumba
Yolimba. Yodalirika. Yotsika mtengo. Yoyenera ntchito iliyonse yomanga.

๐Ÿ›– Malata

10ft โ€” K16,000 yokha

12ft โ€” K19,000 yokha

Gulani mosavuta โ€” imbani kapena WhatsApp: 0995 917 133
Timavomeranso malipiro kudzera munjira izi:

Standard Bank

National Bank

FDH Bank

Airtel Money (Agent Code & Dealer Number zilipo)

Ku Comfort Hardware, cholinga chathu ndi ichi:
Kumanga Chipoka ndi madera ozungulira โ€” nyumba zolimba.
Tiyeni timange limodzi. โœ”๏ธ

Masiku anthu a ntchito ndi Sunday mpaka Friday
Nthawi 8 koloko m'mawa mpaka 5:30 madzulo

29/11/2025

Why pay more when you can build for less โ€” right at your doorstep?
Comfort Hardware is proud to bring you unbeatable prices on top-quality materials right here in Chipoka, Ginnery Trading (opposite Blantyre Stage).

๐Ÿ—๏ธ Akshar Portland Cement โ€” Only K37,500 per bag
Strong. Reliable. Affordable. Perfect for every construction project.

๐Ÿ›– Iron Sheets (Malata)

10ft โ€“ Only K16,000

12ft โ€“ Only K19,000

Order with ease โ€” Call or WhatsApp: 0995 917 133
Payments are accepted through:

Standard Bank

National Bank

FDH Bank

Airtel Money (Agent Code & Dealer Number available)

At Comfort Hardware, our mission is simple:
To build Chipoka and all surrounding areas โ€” one strong structure at a time.
Letโ€™s build together. โœ”๏ธ

17/10/2025

Moni makasitomala athu okondedwa ochokera ku Lifidzi, Chidzanje, Chipoka, Chazima, Nkhwidwi, Ngodzi, Mtakataka, Mua ndi madera ozungulira! ๐Ÿ‘‹

Tili ndi nkhani yabwino kwambiri lero! ๐ŸŽ‰
Malata abweranso ku shopu yathu!

โœ… Topmax Malata

10ft (olimba kwambiri) โ€” K16,000

12ft (olimba kwambiri) โ€” K19,000

๐Ÿงฑ Akshar Cement โ€” tsopano K38,500 yokha pa thumba!

Bwerani msanga kuti mugwiritse ntchito mitengo yabwino kwambiriyi!

๐Ÿ“Tipezeke pa Chipoka Ginnery, moyang'anana ndi Blantyre Stage
๐Ÿ“ž Foni kapena WhatsApp: +265 996 752 209 / 995 917 133

Comfort Hardware โ€” Timange limodzi chitukuko cha dera lathu! ๐Ÿ—๏ธ

17/10/2025

Good morning our valued customers from Lifidzi, Chidzanje, Chipoka, Chazima, Nkhwidwi, Ngodzi, Mtakataka, Mua and surrounding areas!

We are excited to share some great news with you this morning โ€” Malata is back in stock! ๐ŸŽ‰

โœ… Topmax Malata

10ft (Strong quality) โ€” K16,000

12ft (Strong quality) โ€” K19,000

๐Ÿงฑ Akshar Cement โ€” now only K38,500 per bag!

Hurry while stock lasts and take advantage of these unbeatable prices!

๐Ÿ“Find us at the Ginnery, opposite Blantyre Stage (Chipoka)
๐Ÿ“ž Call or WhatsApp: +265 996 752 209/995 917 133

Comfort Hardware โ€” Building our community together!

29/09/2025

Moni moni !

Tinasowana, koma tsopano tabweranso ndi mphamvu!

Tayambaso kupezeka ndi malata a Mkango โ€“ olimba komanso okhalitsa.
๐Ÿ‘‰ 10ft = K17,500 yokha!

Akshar Cement ikadapezekabe pa mtengo wa K37,000 pa thumba!

๐Ÿ“ Tipezeni pa Chipoka Ginnery, moyangโ€™anana ndi Blantyre Stage.
๐Ÿ“ž Imbani +265 996 752 209 kuti mudziwe zambiri kapena kuyitanitsa katundu!

Comfort Hardware โ€“ Kumanga limodzi! ๐Ÿ ๐Ÿ’ช

Ngambwingambwi akshar cement akupezeka pano pa Comfort Hardware pa chipoka ginnery moyang'anana ndi stage ya Blantyre. I...
30/07/2025

Ngambwingambwi akshar cement akupezeka pano pa Comfort Hardware pa chipoka ginnery moyang'anana ndi stage ya Blantyre. Imbani kapena WhatsApp 0995917133

Address

P. O. Box 12
Chipoka

Opening Hours

Monday 08:00 - 17:30
Tuesday 08:00 - 17:30
Wednesday 08:00 - 17:30
Thursday 08:00 - 17:30
Friday 08:00 - 17:30
Sunday 08:00 - 17:30

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Comfort Hardware & One Stop Shop/Solution posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share